Baxxy Mw – Kukoma
Genre Rap

LYRIC
Kukoma

Feat. Simba

Yeaaaaaah [M.O.D]

Ife nde tikumva kukoma
Tikumva kukoma
Ife nde tikumva kukoma
Tikumva kukoma
Iwe kaya zako izo
Kaya zako izo
Iwe kaya zako izo
Kaya zako izo
Ife nde tikumva kukoma
Tikumva kukoma
Ife nde tikumva kukoma
Tikumva kukoma
Iwe kaya zako izo
Kaya zako izo
Iwe kaya zako izo
Kaya zako izo
Dzulo nde tinamva kukoma
Zoti kwada sitimaona
Kuyika stango ndi zi madona
Kuchilla mpaka 5 pa chi corner
Atengana awiri angosowa
Iwenso usowa ukatibhowa
All white phwando la akakowa
Uliwonsewo ukulowa
Nde DJ kweza volume
Ndi spitte patse podium
I'm gassed up ngati petroleum
I’m gassed up ngati petroleum

Ife nde tikumva kukoma
Tikumva kukoma
Ife nde tikumva kukoma
Tikumva kukoma
Iwe kaya zako izo
Kaya zako izo
Iwe kaya zako izo
Kaya zako izo
Ife nde tikumva kukoma
Tikumva kukoma
Ife nde tikumva kukoma
Tikumva kukoma
Iwe kaya zako izo
Kaya zako izo
Iwe kaya zako izo
Kaya zako izo
Ndadyеra mpamba ndaduka
Ndadzimenyetsa ndasupuka
Tinakondwa tinamasuka
Zachitika dzulo nzoyaluka
Timadana ndimafana akaduka
Kuwathotha kuwathira zi maduka
Ndi maluziwa nde timwa zima Shootеr
Ti baller be ngati John Maduka

Ine ndi mponda matiki
My vibe too green, ma pin
Life pon di stage ndima chick
After dat Room 6
Room 6

Ife nde tikumva kukoma
Tikumva kukoma
Ife nde tikumva kukoma
Tikumva kukoma
Iwe kaya zako izo
Kaya zako izo
Iwe kaya zako izo
Kaya zako izo
Ife nde tikumva kukoma
Tikumva kukoma
Ife nde tikumva kukoma
Tikumva kukoma
Iwe kaya zako izo
Kaya zako izo
Iwe kaya zako izo
Kaya zako izo

Leave a Reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *